VOP - Chichewa

VOP - Chichewa

TINGATHE KUKHULUPIRIRA MWA MULUNGU

Tingathe Kukhulupirira Mwa Mulungu?

Nthawi ina Jim anafunsa munthu wosakhulupirira ngati anayamba waganizapo mozama ngati kunjakuno kuli Mulungu kapena ai.

Mwatchutchutchu, munthuyu anati kwa Jim, "zaka za m'mbuyomu pamene mwana wathu woyamba anabadwa; ndinatsala pang'ono kukhulupirira kuti Mulungu aliko; poona kamunthu kakang'ono kangwiro mu kama wake; tidzala take tikugwedera ndi timaso take tikuphethira. Kwa miyezi ingapo ndinali pafupi kusintha maganizo anga akuti kumwamba kulibe Mulungu" Izi zinamudabwitsa Jim.

"Pokaona kamwanako, ndinatsala pang'ono kukwanitsidwa kuti kuyenera kukhala Mulungu". Anapitiriza motero.

Register now

Start your free correspondence course by mail!

Course Content

  • 1.TINGATHE KUKHULUPILIRA MULUNGU
  • 2. TITHA KUKHULUPIRIRA BUKHU LOPATULIKA
  • 3. KODI MOYO WANGA NGOFUNIKA PAMASO PA MULUNGU
  • 4. CHIKONZERO CHA MOYO WANU
  • 5. ULALO WA KU MOYO WOKWANITSIDWA
  • 6. MWAYI WOKHALA MOYO WACHIWIRI
  • 7. ZA TSOGOLO LANU
  • 8 YESU AKADZABWERERA INU
  • 9. KUMWAMBA NDIKO KWANU
  • 10. KODI KUBWERA KWA YESU KWAYANDIKIRA BWANJI
  • 11 - MPHAMVU YODABWITSA MMOYO WANGA
  • 12. MPULUMUTSI WOPEZEKERATU
  • 13. KUCHOKERA KU KUTSUTSIKA NDI CHIMO KUFIKIRA KU WOYERA
  • 14. CHINSINSI CHA PEMPHERO LOYANKHIDWA
  • 15. CHINSINSI CHA CHIMWEMWE
  • 16 - CHINSISNSI CHA MPUMULO WA KUMWAMBA
  • 17. CHINSINSI CHAKUKULA KUPYOLERA MUKUGAWANA
  • 18 - CHINSISNSI CHA OYO WATHANZI
  • 19. KULOWA MMOYO WACHIKHRISTU
  • 20. CHINSINSI CHA KUKULA KUPYOLERA MU CHIYANJANO
  • 21. KODI GULU LINGAKHALE LOLAKWA
  • 22. KODI MULUNGU NDI WACHILUNGAMO
  • 23. KODI GAHENA NDI CHIYANI NANGA ALI KUTI
  • 24. KODI MUNTHU AKAFA CHIMATSATIRAPO NDI CHIYANI
  • 25. KODI TINGAPEZE MPINGO WA MULUNGU LERO
  • 26. KODI MULUNGU ALI NAWO UTHENGA WAPADERA WA NTHAWI YATHU
  • Kuyankha mafunso